1 Mafumu 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a asilikali ake kuti akamenyane ndi anthu amʼmizinda ya Isiraeli. Iwo analanda Iyoni,+ Dani,+ Abele-beti-maaka ndi Kinereti yense komanso dera lonse la Nafitali.
20 Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a asilikali ake kuti akamenyane ndi anthu amʼmizinda ya Isiraeli. Iwo analanda Iyoni,+ Dani,+ Abele-beti-maaka ndi Kinereti yense komanso dera lonse la Nafitali.