1 Mafumu 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno Basa mwana wa Ahiya wa nyumba ya Isakara, anakonzera chiwembu Nadabu ndipo anamupha mumzinda wa Gibitoni,+ womwe unali mʼmanja mwa Afilisiti. Anamupha pa nthawi imene Nadabuyo ndi Aisiraeli onse ankaukira Gibitoni.
27 Ndiyeno Basa mwana wa Ahiya wa nyumba ya Isakara, anakonzera chiwembu Nadabu ndipo anamupha mumzinda wa Gibitoni,+ womwe unali mʼmanja mwa Afilisiti. Anamupha pa nthawi imene Nadabuyo ndi Aisiraeli onse ankaukira Gibitoni.