1 Mafumu 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Basa atangokhala mfumu, anapha anthu onse a mʼnyumba ya Yerobowamu. Sanasiye munthu aliyense wa mʼbanja la Yerobowamu ali ndi moyo. Anapha onse mogwirizana ndi mawu a Yehova amene analankhula kudzera mwa mtumiki wake Ahiya wa ku Silo.+
29 Basa atangokhala mfumu, anapha anthu onse a mʼnyumba ya Yerobowamu. Sanasiye munthu aliyense wa mʼbanja la Yerobowamu ali ndi moyo. Anapha onse mogwirizana ndi mawu a Yehova amene analankhula kudzera mwa mtumiki wake Ahiya wa ku Silo.+