-
1 Mafumu 15:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Izi zinachitika chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha iye komanso chifukwa choti Yerobowamuyo anakwiyitsa kwambiri Yehova Mulungu wa Isiraeli.
-