1 Mafumu 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mʼchaka chachitatu cha Asa mfumu ya Yuda, Basa mwana wa Ahiya anakhala mfumu ya Isiraeli yense ku Tiriza ndipo analamulira kwa zaka 24.+
33 Mʼchaka chachitatu cha Asa mfumu ya Yuda, Basa mwana wa Ahiya anakhala mfumu ya Isiraeli yense ku Tiriza ndipo analamulira kwa zaka 24.+