1 Mafumu 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ ndipo ankayenda mʼnjira ya Yerobowamu ndiponso mʼmachimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha Yerobowamuyo.+
34 Koma iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ ndipo ankayenda mʼnjira ya Yerobowamu ndiponso mʼmachimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha Yerobowamuyo.+