1 Mafumu 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndinakukweza kukuchotsa pafumbi kuti ukhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.+ Koma iwe wakhala ukuyenda mʼnjira ya Yerobowamu nʼkuchimwitsa anthu anga Aisiraeli ndipo andikwiyitsa ndi machimo awo.+
2 “Ndinakukweza kukuchotsa pafumbi kuti ukhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.+ Koma iwe wakhala ukuyenda mʼnjira ya Yerobowamu nʼkuchimwitsa anthu anga Aisiraeli ndipo andikwiyitsa ndi machimo awo.+