1 Mafumu 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Basa, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda ku Tiriza.+ Ndiyeno mwana wake Ela anakhala mfumu mʼmalo mwake.
6 Kenako Basa, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda ku Tiriza.+ Ndiyeno mwana wake Ela anakhala mfumu mʼmalo mwake.