-
1 Mafumu 16:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Komanso Yehova analankhula mawu otsutsa Basa ndi nyumba yake kudzera mwa mneneri Yehu mwana wa Haneni. Anamutsutsa chifukwa cha zoipa zonse zimene Basayo anachita pamaso pa Yehova pomukwiyitsa ndi ntchito ya manja ake ngati mmene anthu a mʼnyumba ya Yerobowamu anachitira ndiponso chifukwa chakuti iye anapha Nadabu.+
-