1 Mafumu 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye atangokhala pampando wachifumu nʼkuyamba kulamulira, anapha anthu onse a mʼnyumba ya Basa. Sanasiye ndi moyo mwamuna* aliyense wa mʼbanja la Basa, kaya wachibale* wake kapena mnzake.
11 Iye atangokhala pampando wachifumu nʼkuyamba kulamulira, anapha anthu onse a mʼnyumba ya Basa. Sanasiye ndi moyo mwamuna* aliyense wa mʼbanja la Basa, kaya wachibale* wake kapena mnzake.