1 Mafumu 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Zimiri anapha anthu onse a mʼnyumba ya Basa, mogwirizana ndi mawu a Yehova otsutsa Basa amene analankhula kudzera mwa mneneri Yehu.+
12 Choncho Zimiri anapha anthu onse a mʼnyumba ya Basa, mogwirizana ndi mawu a Yehova otsutsa Basa amene analankhula kudzera mwa mneneri Yehu.+