1 Mafumu 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anawapha onse chifukwa cha machimo onse amene Basa ndi mwana wake Ela anachita, komanso machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha iwo nʼkukwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mafano awo opanda pake.+
13 Anawapha onse chifukwa cha machimo onse amene Basa ndi mwana wake Ela anachita, komanso machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha iwo nʼkukwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mafano awo opanda pake.+