1 Mafumu 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mʼchaka cha 27 cha Asa mfumu ya Yuda, Zimiri anakhala mfumu ku Tiriza ndipo analamulira masiku 7. Pa nthawiyo nʼkuti asilikali atamanga msasa pafupi ndi mzinda wa Gibitoni,+ umene unali wa Afilisiti, kuti amenyane ndi anthu amumzindawo.
15 Mʼchaka cha 27 cha Asa mfumu ya Yuda, Zimiri anakhala mfumu ku Tiriza ndipo analamulira masiku 7. Pa nthawiyo nʼkuti asilikali atamanga msasa pafupi ndi mzinda wa Gibitoni,+ umene unali wa Afilisiti, kuti amenyane ndi anthu amumzindawo.