1 Mafumu 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Patapita nthawi, asilikali a mumsasawo anamva kuti: “Zimiri anakonzera chiwembu mfumu ndipo waipha.” Choncho tsiku limenelo, Aisiraeli onse omwe anali kumsasako anaveka ufumu Omuri,+ mkulu wa asilikali, kuti akhale mfumu ya Isiraeli.
16 Patapita nthawi, asilikali a mumsasawo anamva kuti: “Zimiri anakonzera chiwembu mfumu ndipo waipha.” Choncho tsiku limenelo, Aisiraeli onse omwe anali kumsasako anaveka ufumu Omuri,+ mkulu wa asilikali, kuti akhale mfumu ya Isiraeli.