1 Mafumu 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zimiri ataona kuti mzindawo walandidwa, anakalowa munsanja yomwe inali panyumba ya mfumu nʼkuyatsa nyumbayo iye ali momwemo, moti anafa.+
18 Zimiri ataona kuti mzindawo walandidwa, anakalowa munsanja yomwe inali panyumba ya mfumu nʼkuyatsa nyumbayo iye ali momwemo, moti anafa.+