1 Mafumu 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anafa chifukwa cha machimo ake popeza anachita zoipa pamaso pa Yehova, anayenda mʼnjira ya Yerobowamu komanso chifukwa cha machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha iyeyo.+
19 Anafa chifukwa cha machimo ake popeza anachita zoipa pamaso pa Yehova, anayenda mʼnjira ya Yerobowamu komanso chifukwa cha machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha iyeyo.+