-
1 Mafumu 16:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma anthu amene ankatsatira Omuri anagonjetsa amene ankatsatira Tibini mwana wa Ginati. Choncho Tibini anafa ndipo Omuri anakhala mfumu.
-