1 Mafumu 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye anagula phiri la Samariya kwa Semeri ndi matalente* awiri asiliva ndipo anamanga mzinda paphiripo. Mzindawo anaupatsa dzina lakuti Samariya*+ lomwe linali dzina la Semeri, mwiniwake* wa phirilo.
24 Iye anagula phiri la Samariya kwa Semeri ndi matalente* awiri asiliva ndipo anamanga mzinda paphiripo. Mzindawo anaupatsa dzina lakuti Samariya*+ lomwe linali dzina la Semeri, mwiniwake* wa phirilo.