1 Mafumu 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye anayenda mʼnjira zonse za Yerobowamu mwana wa Nebati komanso mʼmachimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha iye pokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mafano awo opanda pake.+
26 Iye anayenda mʼnjira zonse za Yerobowamu mwana wa Nebati komanso mʼmachimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha iye pokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mafano awo opanda pake.+