1 Mafumu 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako Omuri, mofanana ndi makolo ake, anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda ku Samariya ndipo mwana wake Ahabu+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
28 Kenako Omuri, mofanana ndi makolo ake, anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda ku Samariya ndipo mwana wake Ahabu+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.