1 Mafumu 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kuwonjezera pamenepo, anamanga guwa lansembe la Baala mʼkachisi wa Baala+ amene iye anamanga ku Samariya.
32 Kuwonjezera pamenepo, anamanga guwa lansembe la Baala mʼkachisi wa Baala+ amene iye anamanga ku Samariya.