1 Mafumu 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika.*+ Iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale mfumu.
33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika.*+ Iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale mfumu.