1 Mafumu 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Eliya*+ wa ku Tisibe, wochokera ku Giliyadi anauza Ahabu+ kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wa Isiraeli amene ndimamʼtumikira, sikubwera mame kapena mvula zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditanena.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:1 Nsanja ya Olonda,4/1/1992, tsa. 1711/1/1990, tsa. 16
17 Eliya*+ wa ku Tisibe, wochokera ku Giliyadi anauza Ahabu+ kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wa Isiraeli amene ndimamʼtumikira, sikubwera mame kapena mvula zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditanena.”+