1 Mafumu 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Uchoke kuno nʼkulowera chakumʼmawa ndipo ukabisale mʼchigwa* cha Keriti chimene chili kumʼmawa kwa Yorodano. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:3 Nsanja ya Olonda,4/1/1992, tsa. 18
3 “Uchoke kuno nʼkulowera chakumʼmawa ndipo ukabisale mʼchigwa* cha Keriti chimene chili kumʼmawa kwa Yorodano.