1 Mafumu 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma patapita masiku angapo,+ mtsinjewo unauma chifukwa mʼdzikomo simunkagwa mvula.