1 Mafumu 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho Eliya ananyamuka nʼkupita ku Zarefati. Atafika pageti la mzindawo anaona mayi wamasiye akutola nkhuni. Ndiyeno anamuitana nʼkumuuza kuti: “Mundipatseko madzi pangʼono mʼkapu kuti ndimwe.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:10 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 13
10 Choncho Eliya ananyamuka nʼkupita ku Zarefati. Atafika pageti la mzindawo anaona mayi wamasiye akutola nkhuni. Ndiyeno anamuitana nʼkumuuza kuti: “Mundipatseko madzi pangʼono mʼkapu kuti ndimwe.”+