-
1 Mafumu 17:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ufa umene unali mumtsuko waukulu sunathe, ndipo mafuta amene anali mumtsuko waungʼono sanathe, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena kudzera mwa Eliya.
-