1 Mafumu 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako mwana wamwamuna wa mayiyo anadwala. Matenda ake anakula kwambiri mpaka anamwalira.+