1 Mafumu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zitatero, mayiyo anauza Eliya kuti: “Ndakulakwirani chiyani inu munthu wa Mulungu woona? Kodi mwabwera kudzandikumbutsa zimene ndinalakwitsa komanso kudzapha mwana wanga?”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:18 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 15
18 Zitatero, mayiyo anauza Eliya kuti: “Ndakulakwirani chiyani inu munthu wa Mulungu woona? Kodi mwabwera kudzandikumbutsa zimene ndinalakwitsa komanso kudzapha mwana wanga?”+