1 Mafumu 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Eliya anamuuza kuti: “Bweretsani mwana wanuyo.” Ndiyeno anatenga mwanayo mʼmanja mwa mayi ake nʼkupita naye kuchipinda chapadenga chimene Eliyayo ankakhala, ndipo anamugoneka pabedi lake.+
19 Koma Eliya anamuuza kuti: “Bweretsani mwana wanuyo.” Ndiyeno anatenga mwanayo mʼmanja mwa mayi ake nʼkupita naye kuchipinda chapadenga chimene Eliyayo ankakhala, ndipo anamugoneka pabedi lake.+