-
1 Mafumu 17:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndiyeno anakumbatira mwanayo katatu ali pabedipo nʼkufuulira Yehova kuti: “Inu Yehova Mulungu wanga, chonde chititsani kuti moyo wa mwanayu ubwerere.”
-