1 Mafumu 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Eliya anatenga mwanayo nʼkutsika naye kuchokera mʼchipinda chapadenga chija ndipo anapita naye kwa mayi ake. Ndiyeno anati: “Mwana wanu uja tsopano ali moyo.”+
23 Eliya anatenga mwanayo nʼkutsika naye kuchokera mʼchipinda chapadenga chija ndipo anapita naye kwa mayi ake. Ndiyeno anati: “Mwana wanu uja tsopano ali moyo.”+