1 Mafumu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Patapita nthawi, mʼchaka chachitatu,+ Eliya anamva mawu a Yehova akuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula mʼdzikoli.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:1 Nsanja ya Olonda,4/1/2008, tsa. 194/1/1992, tsa. 17
18 Patapita nthawi, mʼchaka chachitatu,+ Eliya anamva mawu a Yehova akuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula mʼdzikoli.”+