1 Mafumu 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Eliya anapita kukaonekera kwa Ahabu. Pa nthawiyi nʼkuti njala itafika poipa kwambiri+ ku Samariya.
2 Choncho Eliya anapita kukaonekera kwa Ahabu. Pa nthawiyi nʼkuti njala itafika poipa kwambiri+ ku Samariya.