1 Mafumu 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo pamene Yezebeli+ ankapha aneneri a Yehova, Obadiya anatenga aneneri 100 nʼkuwagawa mʼmagulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga nʼkumawapatsa chakudya ndi madzi.) 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:4 Nsanja ya Olonda,10/1/2006, tsa. 20
4 Ndipo pamene Yezebeli+ ankapha aneneri a Yehova, Obadiya anatenga aneneri 100 nʼkuwagawa mʼmagulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga nʼkumawapatsa chakudya ndi madzi.)