1 Mafumu 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tikasiyana pano, mzimu wa Yehova ubwera nʼkukutengani+ kupita nanu kumalo amene ine sindingawadziwe. Ndiye ndikakauza Ahabu koma iyeyo osakupezani, adzandipha ndithu. Komatu ine mtumiki wanu ndakhala ndikuopa Yehova kuyambira ndili mwana.
12 Tikasiyana pano, mzimu wa Yehova ubwera nʼkukutengani+ kupita nanu kumalo amene ine sindingawadziwe. Ndiye ndikakauza Ahabu koma iyeyo osakupezani, adzandipha ndithu. Komatu ine mtumiki wanu ndakhala ndikuopa Yehova kuyambira ndili mwana.