1 Mafumu 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi inu mbuye wanga simunamve zimene ndinachita pamene Yezebeli ankapha aneneri a Yehova? Ndinabisa aneneri 100 a Yehova mʼphanga. Ndinawagawa mʼmagulu awiri a aneneri 50 gulu lililonse ndipo ndinkawapatsa chakudya ndi madzi.+
13 Kodi inu mbuye wanga simunamve zimene ndinachita pamene Yezebeli ankapha aneneri a Yehova? Ndinabisa aneneri 100 a Yehova mʼphanga. Ndinawagawa mʼmagulu awiri a aneneri 50 gulu lililonse ndipo ndinkawapatsa chakudya ndi madzi.+