-
1 Mafumu 18:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Koma Eliya anati: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wamoyo amene ndimamʼtumikira, lero ndionekera kwa Ahabu.”
-