1 Mafumu 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Eliya anayankha kuti: “Ine sindinabweretse mavuto mu Isiraeli, koma inuyo ndi nyumba ya bambo anu. Chifukwa mwasiya kutsatira malamulo a Yehova nʼkuyamba kutsatira Abaala.+
18 Eliya anayankha kuti: “Ine sindinabweretse mavuto mu Isiraeli, koma inuyo ndi nyumba ya bambo anu. Chifukwa mwasiya kutsatira malamulo a Yehova nʼkuyamba kutsatira Abaala.+