1 Mafumu 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano sonkhanitsani Aisiraeli onse kuti ndikakumane nawo paphiri la Karimeli.+ Musonkhanitsenso aneneri 450 a Baala ndi aneneri 400 a mzati wopatulika,*+ amene amadya patebulo la Yezebeli.”
19 Tsopano sonkhanitsani Aisiraeli onse kuti ndikakumane nawo paphiri la Karimeli.+ Musonkhanitsenso aneneri 450 a Baala ndi aneneri 400 a mzati wopatulika,*+ amene amadya patebulo la Yezebeli.”