1 Mafumu 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pofika masana, Eliya anayamba kuwaseka nʼkumanena kuti: “Muitaneni mokuwa kwambiri chifukwa iye ndi mulungu.+ Mwina akuganizira zinazake kapena wapita kuchimbudzi.* Mwinanso wagona ndipo akufunika kumudzutsa.” 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:27 Tsanzirani, tsa. 88 Nsanja ya Olonda,1/1/2008, tsa. 20
27 Pofika masana, Eliya anayamba kuwaseka nʼkumanena kuti: “Muitaneni mokuwa kwambiri chifukwa iye ndi mulungu.+ Mwina akuganizira zinazake kapena wapita kuchimbudzi.* Mwinanso wagona ndipo akufunika kumudzutsa.”