-
1 Mafumu 18:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Iwo anayamba kuitana mokuwa kwambiri nʼkumadzichekacheka ndi mipeni ndi mikondo ingʼonoingʼono mogwirizana ndi mwambo wawo, mpaka magazi anayamba kuyenderera pamatupi awo.
-