1 Mafumu 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo anapitiriza kuchita ngati amisala* mpaka dzuwa linapendeka. Anapitirizabe mpaka nthawi yopereka nsembe yambewu yamadzulo. Koma sipanamveke mawu alionse ndiponso palibe amene anayankha kapena kuwamvera.+
29 Iwo anapitiriza kuchita ngati amisala* mpaka dzuwa linapendeka. Anapitirizabe mpaka nthawi yopereka nsembe yambewu yamadzulo. Koma sipanamveke mawu alionse ndiponso palibe amene anayankha kapena kuwamvera.+