-
1 Mafumu 18:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Ndiyeno pa nthawi yopereka nsembe yambewu yamadzulo,+ mneneri Eliya anayandikira guwa lansembelo nʼkunena kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Abulahamu,+ Isaki+ ndi Isiraeli, lero zidziwike kuti inu ndinu Mulungu mu Isiraeli ndiponso kuti ine ndine mtumiki wanu, komanso kuti ndachita zonsezi potsatira mawu anu.+
-