1 Mafumu 18:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyankheni Yehova, ndiyankheni, kuti anthu awa adziwe kuti inu Yehova ndinu Mulungu woona ndiponso kuti mukubweza mitima yawo kuti abwerere kwa inu.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:37 Tsanzirani, tsa. 90 Nsanja ya Olonda,10/1/2010, ptsa. 4-51/1/2008, tsa. 20
37 Ndiyankheni Yehova, ndiyankheni, kuti anthu awa adziwe kuti inu Yehova ndinu Mulungu woona ndiponso kuti mukubweza mitima yawo kuti abwerere kwa inu.”+