1 Mafumu 18:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Atatero, moto wa Yehova unatsika nʼkutentha nsembe yopsereza ija,+ nkhuni, miyala ndi fumbi lomwe. Unaumitsanso madzi amene anali mʼngalande aja.+
38 Atatero, moto wa Yehova unatsika nʼkutentha nsembe yopsereza ija,+ nkhuni, miyala ndi fumbi lomwe. Unaumitsanso madzi amene anali mʼngalande aja.+