-
1 Mafumu 18:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Anthu onsewo ataona zimenezo, nthawi yomweyo anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo kufika pansi, ndipo ananena kuti: “Mulungu woona ndi Yehova! Mulungu woona ndi Yehova!”
-