1 Mafumu 18:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Gwirani aneneri a Baala! Muonetsetse kuti pasapezeke wothawa!” Nthawi yomweyo anawagwira ndipo Eliya anatsetserekera nawo kumtsinje* wa Kisoni+ nʼkukawapha kumeneko.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:40 Tsanzirani, ptsa. 90-91 Nsanja ya Olonda,1/1/2008, ptsa. 20-21
40 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Gwirani aneneri a Baala! Muonetsetse kuti pasapezeke wothawa!” Nthawi yomweyo anawagwira ndipo Eliya anatsetserekera nawo kumtsinje* wa Kisoni+ nʼkukawapha kumeneko.+