1 Mafumu 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Eliya anachita mantha moti ananyamuka nʼkuyamba kuthawa kuti apulumutse moyo wake.+ Atafika ku Beere-seba+ wa ku Yuda,+ anasiya mtumiki wake kumeneko. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:3 Tsanzirani, ptsa. 101-102 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, ptsa. 19-20
3 Choncho Eliya anachita mantha moti ananyamuka nʼkuyamba kuthawa kuti apulumutse moyo wake.+ Atafika ku Beere-seba+ wa ku Yuda,+ anasiya mtumiki wake kumeneko.