1 Mafumu 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anagona pansi pa kamtengo kaja mpaka tulo tinamʼpeza. Mwadzidzidzi kunabwera mngelo ndipo anamukhudza+ nʼkumuuza kuti: “Dzuka udye.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:5 Tsanzirani, tsa. 103 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, tsa. 20
5 Kenako anagona pansi pa kamtengo kaja mpaka tulo tinamʼpeza. Mwadzidzidzi kunabwera mngelo ndipo anamukhudza+ nʼkumuuza kuti: “Dzuka udye.”+